Mateyu 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano anayandikira ku Yerusalemu, ndipo atafika ku Betefage paphiri la Maolivi, Yesu anatuma ophunzira awiri+ Luka 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsopano atayandikira ku Betefage ndi Betaniya paphiri lotchedwa phiri la Maolivi,+ anatumiza ophunzira ake awiri.+
21 Tsopano anayandikira ku Yerusalemu, ndipo atafika ku Betefage paphiri la Maolivi, Yesu anatuma ophunzira awiri+
29 Tsopano atayandikira ku Betefage ndi Betaniya paphiri lotchedwa phiri la Maolivi,+ anatumiza ophunzira ake awiri.+