Mateyu 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano anayandikira ku Yerusalemu, ndipo atafika ku Betefage paphiri la Maolivi, Yesu anatuma ophunzira awiri+ Maliko 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano pamene anali kuyandikira Yerusalemu, Betefage ndi Betaniya,+ ali paphiri la Maolivi, anatumiza ophunzira ake awiri+
21 Tsopano anayandikira ku Yerusalemu, ndipo atafika ku Betefage paphiri la Maolivi, Yesu anatuma ophunzira awiri+
11 Tsopano pamene anali kuyandikira Yerusalemu, Betefage ndi Betaniya,+ ali paphiri la Maolivi, anatumiza ophunzira ake awiri+