Mateyu 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yesu anawayankha kuti: “Anzake a mkwati samva chisoni ngati mkwatiyo+ ali nawo limodzi, si choncho kodi? Koma masiku adzafika pamene mkwatiyo adzachotsedwa+ pakati pawo, ndipo pa nthawiyo adzasala kudya.+ Luka 5:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Koma masiku adzafika pamene mkwati+ adzachotsedwa pakati pawo.+ Pamenepo iwo adzasala kudya masiku amenewo.”+ Yohane 8:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Atate wanu Abulahamu anali wosangalala poyembekezera kuona tsiku langa,+ ndipo analiona moti anakondwera.”+
15 Yesu anawayankha kuti: “Anzake a mkwati samva chisoni ngati mkwatiyo+ ali nawo limodzi, si choncho kodi? Koma masiku adzafika pamene mkwatiyo adzachotsedwa+ pakati pawo, ndipo pa nthawiyo adzasala kudya.+
35 Koma masiku adzafika pamene mkwati+ adzachotsedwa pakati pawo.+ Pamenepo iwo adzasala kudya masiku amenewo.”+
56 Atate wanu Abulahamu anali wosangalala poyembekezera kuona tsiku langa,+ ndipo analiona moti anakondwera.”+