Mateyu 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mbuye wakeyo anamuyankha kuti, ‘Wachita bwino kwambiri, kapolo wabwino ndi wokhulupirika iwe!+ Unakhulupirika+ pa zinthu zochepa. Ndikuika kuti udziyang’anira zinthu zambiri.+ Sangalala+ limodzi ndi ine mbuye wako.’ Luka 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu wokhulupirika pa chinthu chaching’ono alinso wokhulupirika pa chinthu chachikulu, ndipo munthu wosalungama pa chinthu chaching’ono alinso wosalungama pa chinthu chachikulu.+ Chivumbulutso 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndipo amene wapambana pa nkhondo ndi kutsatira zochita zanga kufikira mapeto,+ ndidzamupatsa ulamuliro pa mitundu ya anthu.+
21 Mbuye wakeyo anamuyankha kuti, ‘Wachita bwino kwambiri, kapolo wabwino ndi wokhulupirika iwe!+ Unakhulupirika+ pa zinthu zochepa. Ndikuika kuti udziyang’anira zinthu zambiri.+ Sangalala+ limodzi ndi ine mbuye wako.’
10 Munthu wokhulupirika pa chinthu chaching’ono alinso wokhulupirika pa chinthu chachikulu, ndipo munthu wosalungama pa chinthu chaching’ono alinso wosalungama pa chinthu chachikulu.+
26 Ndipo amene wapambana pa nkhondo ndi kutsatira zochita zanga kufikira mapeto,+ ndidzamupatsa ulamuliro pa mitundu ya anthu.+