Deuteronomo 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mlendo+ ungamulipiritse chiwongoladzanja, koma m’bale wako usamulipiritse chiwongoladzanja,+ kuti Yehova Mulungu wako akudalitse pa zochita zako zonse m’dziko limene ukupita kukalitenga kukhala lako.+ Mateyu 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyetu ukanasungitsa ndalama zanga zasilivazi kwa osunga ndalama, ndipo ine pobwera ndikanalandira ndalama zangazo limodzi ndi chiwongoladzanja chake.+
20 Mlendo+ ungamulipiritse chiwongoladzanja, koma m’bale wako usamulipiritse chiwongoladzanja,+ kuti Yehova Mulungu wako akudalitse pa zochita zako zonse m’dziko limene ukupita kukalitenga kukhala lako.+
27 Ndiyetu ukanasungitsa ndalama zanga zasilivazi kwa osunga ndalama, ndipo ine pobwera ndikanalandira ndalama zangazo limodzi ndi chiwongoladzanja chake.+