Genesis 46:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamapeto pake Isiraeli anauza Yosefe kuti: “Ndingathe kufa+ tsopano chifukwa ndaona nkhope yako, popeza ukadali ndi moyo.” Yesaya 57:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye amalowa mumtendere.+ Aliyense woyenda mowongoka+ amapita kukapuma+ m’manda.*+
30 Pamapeto pake Isiraeli anauza Yosefe kuti: “Ndingathe kufa+ tsopano chifukwa ndaona nkhope yako, popeza ukadali ndi moyo.”