Salimo 119:99 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 99 Ndakhala wozindikira kwambiri kuposa aphunzitsi anga,+Chifukwa ndimasinkhasinkha zikumbutso zanu.+ Mateyu 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano Yesu atatsiriza mawu amenewa, khamu la anthulo linakhudzidwa moti linadabwa+ ndi kaphunzitsidwe kake, Maliko 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mmenemo anthu anadabwa kwambiri ndi kaphunzitsidwe kake,+ chifukwa anali kuwaphunzitsa monga munthu wokhala ndi ulamuliro, osati monga alembi.+ Yohane 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Ayudawo anayamba kudabwa ndi kufunsa kuti: “Kodi munthu ameneyu zolembazi anazidziwa bwanji,+ popeza sanapite kusukulu?”+
99 Ndakhala wozindikira kwambiri kuposa aphunzitsi anga,+Chifukwa ndimasinkhasinkha zikumbutso zanu.+
28 Tsopano Yesu atatsiriza mawu amenewa, khamu la anthulo linakhudzidwa moti linadabwa+ ndi kaphunzitsidwe kake,
22 Mmenemo anthu anadabwa kwambiri ndi kaphunzitsidwe kake,+ chifukwa anali kuwaphunzitsa monga munthu wokhala ndi ulamuliro, osati monga alembi.+
15 Pamenepo Ayudawo anayamba kudabwa ndi kufunsa kuti: “Kodi munthu ameneyu zolembazi anazidziwa bwanji,+ popeza sanapite kusukulu?”+