Mateyu 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo ananyamuka n’kupita kwawo. Maliko 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo munthuyo anadzuka, ndipo nthawi yomweyo ananyamula machira akewo ndi kuyenda yekha pamaso pa onse,+ moti onsewo anadabwa kwambiri, ndipo anatamanda Mulungu kuti: “Zoterezi sitinazionepo.”+ Machitidwe 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho atawonjezera kuwaopseza, anawamasula, pakuti sanapeze chifukwa chilichonse chowapatsira chilango. Komanso anaopa anthu,+ pakuti onse anali kutamanda Mulungu chifukwa cha zimene zinachitikazo. Agalatiya 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho anthuwo anayamba kulemekeza+ Mulungu chifukwa cha ine.
12 Pamenepo munthuyo anadzuka, ndipo nthawi yomweyo ananyamula machira akewo ndi kuyenda yekha pamaso pa onse,+ moti onsewo anadabwa kwambiri, ndipo anatamanda Mulungu kuti: “Zoterezi sitinazionepo.”+
21 Choncho atawonjezera kuwaopseza, anawamasula, pakuti sanapeze chifukwa chilichonse chowapatsira chilango. Komanso anaopa anthu,+ pakuti onse anali kutamanda Mulungu chifukwa cha zimene zinachitikazo.