Miyambo 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Woyamba kufotokoza mbali yake pa mlandu amaoneka ngati wolondola,+ koma mnzake amabwera n’kumufufuzafufuza.+ Aroma 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 kodi iwe wophunzitsa enawe, sudziphunzitsa wekha?+ Iwe amene umalalikira kuti “Usabe,”+ umabanso kodi?+
17 Woyamba kufotokoza mbali yake pa mlandu amaoneka ngati wolondola,+ koma mnzake amabwera n’kumufufuzafufuza.+
21 kodi iwe wophunzitsa enawe, sudziphunzitsa wekha?+ Iwe amene umalalikira kuti “Usabe,”+ umabanso kodi?+