Deuteronomo 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale kuti wapeza chuma atagulitsa katundu wa makolo ake, gawo la chakudya chake lizikhala lofanana ndi ansembe onse.+ 1 Akorinto 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ngati wina mwa osakhulupirira wakuitanani ndipo mwapita, kadyeni zonse zimene wakupatsani,+ popanda kufunsa mafunso poopera chikumbumtima chanu.+ Agalatiya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso, aliyense amene akuphunzitsidwa mawuwo+ agawane+ zinthu zonse zabwino ndi amene akumuphunzitsayo.+
8 Ngakhale kuti wapeza chuma atagulitsa katundu wa makolo ake, gawo la chakudya chake lizikhala lofanana ndi ansembe onse.+
27 Ngati wina mwa osakhulupirira wakuitanani ndipo mwapita, kadyeni zonse zimene wakupatsani,+ popanda kufunsa mafunso poopera chikumbumtima chanu.+
6 Komanso, aliyense amene akuphunzitsidwa mawuwo+ agawane+ zinthu zonse zabwino ndi amene akumuphunzitsayo.+