Levitiko 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma nsembe yambewu iliyonse yothira mafuta+ kapena youma+ izikhala ya ana onse aamuna a Aroni, azigawana mofanana. Luka 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho khalani m’nyumba yamtendereyo.+ Muzidya ndi kumwa zimene angakupatseni,+ chifukwa wantchito ayenera kulandira malipiro ake.+ Musamachoke kumene mwafikirako n’kupita kunyumba zina.+ 1 Timoteyo 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti lemba limati: “Usamange ng’ombe pakamwa pamene ikupuntha mbewu.”+ Komanso limati: “Wantchito ayenera kulandira malipiro ake.”+
10 Koma nsembe yambewu iliyonse yothira mafuta+ kapena youma+ izikhala ya ana onse aamuna a Aroni, azigawana mofanana.
7 Choncho khalani m’nyumba yamtendereyo.+ Muzidya ndi kumwa zimene angakupatseni,+ chifukwa wantchito ayenera kulandira malipiro ake.+ Musamachoke kumene mwafikirako n’kupita kunyumba zina.+
18 Pakuti lemba limati: “Usamange ng’ombe pakamwa pamene ikupuntha mbewu.”+ Komanso limati: “Wantchito ayenera kulandira malipiro ake.”+