Luka 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti aliyense wochita manyazi ndi ine, komanso ndi mawu anga, Mwana wa munthu adzachitanso naye manyazi akadzafika mu ulemerero wake, wa Atate wake ndi wa angelo oyera.+ 2 Timoteyo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tikapitiriza kupirira, tidzalamuliranso limodzi ndi iye monga mafumu.+ Tikamukana,+ iyenso adzatikana, 1 Yohane 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Aliyense amene amakana Mwana sangakhale pa ubwenzi ndi Atate.+ Amene wavomereza+ Mwana amakhalanso pa ubwenzi ndi Atate.+
26 Pakuti aliyense wochita manyazi ndi ine, komanso ndi mawu anga, Mwana wa munthu adzachitanso naye manyazi akadzafika mu ulemerero wake, wa Atate wake ndi wa angelo oyera.+
12 Tikapitiriza kupirira, tidzalamuliranso limodzi ndi iye monga mafumu.+ Tikamukana,+ iyenso adzatikana,
23 Aliyense amene amakana Mwana sangakhale pa ubwenzi ndi Atate.+ Amene wavomereza+ Mwana amakhalanso pa ubwenzi ndi Atate.+