Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Iwowa anabadwa kwa Mulungu, osati kudzera m’magazi kapena m’chifuniro cha thupi, kapena chifuniro cha anthu.+

  • 1 Akorinto 15:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Koma abale, ndikunenetsa kuti mnofu ndi magazi sizingalowe ufumu wa Mulungu.+ Komanso chowonongeka sichingalandire kusawonongeka.+

  • 2 Akorinto 5:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho ngati aliyense ali wogwirizana ndi Khristu, iye ndi cholengedwa chatsopano.+ Zinthu zakale zinatha,+ ndipo pali zatsopano.+

  • Agalatiya 6:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakuti kudulidwa kapena kusadulidwa si kanthu,+ koma chofunika ndi kukhala wolengedwa mwatsopano.+

  • 1 Petulo 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Atamandike Mulungu amenenso ndi Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti mwachifundo chake chachikulu, anatibereka mwatsopano+ kuti tikhale ndi chiyembekezo cha moyo+ mwa kuukitsidwa+ kwa Yesu Khristu.

  • 1 Petulo 1:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pakuti inu mwabadwa mwatsopano,+ osati kuchokera m’mbewu yotha kuwonongeka,+ koma m’mbewu+ yosatha kuwonongeka,+ kudzera m’mawu+ a Mulungu wamoyo ndi wamuyaya.+

  • 1 Yohane 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Aliyense amene ali mwana wa Mulungu sapitiriza kuchita tchimo,+ chifukwa mbewu ya Mulungu yopatsa moyo imakhalabe mwa munthu ameneyo, ndipo sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo, chifukwa ndi mwana wa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena