Aroma 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti mzimuwo+ umachitira umboni+ limodzi ndi mzimu wathu+ kuti ndife ana a Mulungu.+ 2 Akorinto 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Ndidzakhala atate wanu,+ ndipo inu mudzakhala ana anga aamuna ndi aakazi,’+ watero Yehova Wamphamvuyonse.”+ Aefeso 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti anatisankhiratu+ kuti adzatitenga+ kukhala ana ake+ kudzera mwa Yesu Khristu, malinga ndi zomukomera iyeyo ndiponso chifuniro chake.+ 1 Yohane 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taganizirani za chikondi chachikulu+ chimene Atate watisonyeza. Watitchula kuti ndife ana a Mulungu,+ ndipo ndifedi ana ake. N’chifukwa chake dziko+ silitidziwa, pakuti silimudziwa iyeyo.+
18 “‘Ndidzakhala atate wanu,+ ndipo inu mudzakhala ana anga aamuna ndi aakazi,’+ watero Yehova Wamphamvuyonse.”+
5 Pakuti anatisankhiratu+ kuti adzatitenga+ kukhala ana ake+ kudzera mwa Yesu Khristu, malinga ndi zomukomera iyeyo ndiponso chifuniro chake.+
3 Taganizirani za chikondi chachikulu+ chimene Atate watisonyeza. Watitchula kuti ndife ana a Mulungu,+ ndipo ndifedi ana ake. N’chifukwa chake dziko+ silitidziwa, pakuti silimudziwa iyeyo.+