Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Panamvekanso mawu+ ochokera kumwamba onena kuti: “Uyu ndiye Mwana wanga+ wokondedwa,+ amene ndimakondwera naye.”+

  • Mateyu 17:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mawu ake adakali m’kamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba, ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye,+ muzimumvera.”+

  • Maliko 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo panamveka mawu ochokera kumwamba akuti: “Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa, ndimakondwera nawe.”+

  • Maliko 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamenepo kunachita mtambo ndipo unawaphimba. Kenako mumtambomo munatuluka mawu+ akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga+ wokondedwa, muzimumvera.”+

  • Luka 3:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pamenepo mzimu woyera wooneka ngati nkhunda unatsika kudzamutera. Ndiyeno panamveka mawu ochokera kumwamba, akuti: “Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa, ndimakondwera nawe.”+

  • Luka 9:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Ndiyeno mawu+ anatuluka mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga, amene ndinam’sankha.+ Mumvereni.”+

  • 2 Petulo 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pakuti iye analandira ulemu ndi ulemerero kuchokera kwa Mulungu Atate,+ pamene mawu anamveka kwa iye kuchokera mu ulemerero waukulu, kuti: “Uyu ndiye mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena