Yesaya 60:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Wamng’ono adzasanduka anthu 1,000, ndipo wochepa adzasanduka mtundu wamphamvu.+ Ineyo Yehova ndidzafulumizitsa zimenezi pa nthawi yake.”+ Machitidwe 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma anthu ambiri amene anamvetsera mawu awo anakhulupirira,+ ndipo chiwerengero cha amuna chinakwana pafupifupi 5,000.+ Machitidwe 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso okhulupirira Ambuye anapitiriza kuwonjezeka, chifukwa amuna ndi akazi ambirimbiri anakhala ophunzira.+
22 Wamng’ono adzasanduka anthu 1,000, ndipo wochepa adzasanduka mtundu wamphamvu.+ Ineyo Yehova ndidzafulumizitsa zimenezi pa nthawi yake.”+
4 Koma anthu ambiri amene anamvetsera mawu awo anakhulupirira,+ ndipo chiwerengero cha amuna chinakwana pafupifupi 5,000.+
14 Komanso okhulupirira Ambuye anapitiriza kuwonjezeka, chifukwa amuna ndi akazi ambirimbiri anakhala ophunzira.+