Machitidwe 2:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choncho amene analandira mawu akewo ndi mtima wonse anabatizidwa,+ moti tsiku limenelo chiwerengero cha ophunzirawo chinawonjezeka ndi anthu pafupifupi 3,000.+ Machitidwe 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo mawu a Mulungu anapitiriza kufalikira ponseponse.+ Chiwerengero cha ophunzira chinali kuwonjezeka kwambiri mu Yerusalemu.+ Ndipo ansembe ambirimbiri+ anakhala okhulupirira.+
41 Choncho amene analandira mawu akewo ndi mtima wonse anabatizidwa,+ moti tsiku limenelo chiwerengero cha ophunzirawo chinawonjezeka ndi anthu pafupifupi 3,000.+
7 Pamenepo mawu a Mulungu anapitiriza kufalikira ponseponse.+ Chiwerengero cha ophunzira chinali kuwonjezeka kwambiri mu Yerusalemu.+ Ndipo ansembe ambirimbiri+ anakhala okhulupirira.+