Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano Saulo anayamba kuzunza mpingo mwankhanza. Anali kulowa m’nyumba ndi nyumba, ndi kukokera panja amuna ndi akazi omwe, n’kukawaponya m’ndende.+

  • Machitidwe 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 kukamupempha zikalata za chilolezo zopita nazo kumasunagoge a ku Damasiko. Anapempha zikalatazo kuti akakapeza wina aliyense wotsatira Njirayo,*+ mwamuna kapena mkazi, akabwere naye ku Yerusalemu ali womangidwa.

  • 1 Timoteyo 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Anatero ngakhale kuti kale ndinali wonyoza Mulungu, wozunza anthu ake+ ndiponso wachipongwe.+ Komabe anandichitira chifundo+ chifukwa ndinali wosadziwa+ ndi wopanda chikhulupiriro.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena