Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 10:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iwo anati: “Tachokera kwa Koneliyo, kapitawo wa asilikali. Iye ndi munthu wolungama ndi woopa Mulungu,+ amene mtundu wonse wa Ayuda umamuyamikira.+ Mngelo woyera anamupatsa malangizo a Mulungu kuti atume anthu kudzakutengani kuti mupite kunyumba kwake, akamve zimene inu mukanene.”

  • 1 Timoteyo 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Komanso, akhale woti ngakhale anthu akunja* akumuchitira umboni wabwino,+ kuti asatonzedwe ndi kukodwa mumsampha+ wa Mdyerekezi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena