Machitidwe 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye anati: “Ayuda agwirizana zoti akupempheni kuti mupititse Paulo kubwalo la Khoti Lalikulu la Ayuda mawa, ngati kuti iwo akufuna kumvetsa bwino za iye.+
20 Iye anati: “Ayuda agwirizana zoti akupempheni kuti mupititse Paulo kubwalo la Khoti Lalikulu la Ayuda mawa, ngati kuti iwo akufuna kumvetsa bwino za iye.+