Machitidwe 16:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma Paulo anawauza kuti: “Iwo atikwapula pamaso pa anthu ndi kutiponya m’ndende popanda kuzenga mlandu wathu, chikhalirecho ndife Aroma.+ Kodi tsopano akutitulutsa mseri? Ayi, zimenezo sizitheka! Abwere eniakewo adzatitulutse okha.” Machitidwe 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma atamugoneka kuti amukwapule, Paulo anafunsa kapitawo wa asilikali amene anali ataima pamenepo kuti: “Kodi anthu inu, malamulo amakulolani kukwapula munthu amene ndi Mroma,+ mlandu wake usanazengedwe?”
37 Koma Paulo anawauza kuti: “Iwo atikwapula pamaso pa anthu ndi kutiponya m’ndende popanda kuzenga mlandu wathu, chikhalirecho ndife Aroma.+ Kodi tsopano akutitulutsa mseri? Ayi, zimenezo sizitheka! Abwere eniakewo adzatitulutse okha.”
25 Koma atamugoneka kuti amukwapule, Paulo anafunsa kapitawo wa asilikali amene anali ataima pamenepo kuti: “Kodi anthu inu, malamulo amakulolani kukwapula munthu amene ndi Mroma,+ mlandu wake usanazengedwe?”