Machitidwe 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Patapita masiku asanu, kunafika mkulu wa ansembe Hananiya+ pamodzi ndi akulu ena, komanso munthu wina wodziwa kulankhula, dzina lake Teritulo. Iwo ananeneza+ Paulo kwa bwanamkubwa.+ Machitidwe 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ine ndinawayankha kuti, Aroma sachita zinthu mwa njira imeneyo. Iwo sapereka munthu m’manja mwa omuneneza pongofuna kuwakondweretsa, munthu wonenezedwayo+ asanapatsidwe mwayi woonana pamasom’pamaso ndi omunenezawo kuti alankhule mawu odziteteza pa mlanduwo.
24 Patapita masiku asanu, kunafika mkulu wa ansembe Hananiya+ pamodzi ndi akulu ena, komanso munthu wina wodziwa kulankhula, dzina lake Teritulo. Iwo ananeneza+ Paulo kwa bwanamkubwa.+
16 Koma ine ndinawayankha kuti, Aroma sachita zinthu mwa njira imeneyo. Iwo sapereka munthu m’manja mwa omuneneza pongofuna kuwakondweretsa, munthu wonenezedwayo+ asanapatsidwe mwayi woonana pamasom’pamaso ndi omunenezawo kuti alankhule mawu odziteteza pa mlanduwo.