Salimo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amalankhulana zabodza.+Amalankhulana ndi milomo yoshashalika+ komanso ndi mitima iwiri.+ Salimo 55:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mawu a pakamwa pake ndi osalala ngati mafuta a mkaka,+Koma mtima wake umakonda ndewu.+Mawu ake ndi osalala ngati mafuta,+Koma ali ngati lupanga lakuthwa.+ Miyambo 26:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Lilime lonama limadana ndi amene lam’pweteka,+ ndipo pakamwa polankhula zabwino mokokomeza pamabweretsa chiwonongeko.+
21 Mawu a pakamwa pake ndi osalala ngati mafuta a mkaka,+Koma mtima wake umakonda ndewu.+Mawu ake ndi osalala ngati mafuta,+Koma ali ngati lupanga lakuthwa.+
28 Lilime lonama limadana ndi amene lam’pweteka,+ ndipo pakamwa polankhula zabwino mokokomeza pamabweretsa chiwonongeko.+