Machitidwe 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ngati nkhani yake ili yokhudza mikangano pa mawu, mayina+ ndi chilamulo+ chanu, zimenezo muthane nazo nokha. Ine sindikufuna kuti ndikhale woweruza nkhani zoterezi.” Machitidwe 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kumeneko ndinapeza kuti akumuimba mlandu pa nkhani zokhudza Chilamulo chawo.+ Koma sanapezeke ndi mlandu uliwonse woyenera chilango cha imfa kapena kuponyedwa m’ndende.+
15 Koma ngati nkhani yake ili yokhudza mikangano pa mawu, mayina+ ndi chilamulo+ chanu, zimenezo muthane nazo nokha. Ine sindikufuna kuti ndikhale woweruza nkhani zoterezi.”
29 Kumeneko ndinapeza kuti akumuimba mlandu pa nkhani zokhudza Chilamulo chawo.+ Koma sanapezeke ndi mlandu uliwonse woyenera chilango cha imfa kapena kuponyedwa m’ndende.+