Machitidwe 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iwo anali kumumvetsera mpaka pa mawu amenewa. Kenako anafuula kuti: “Munthu ameneyu asapezekenso padziko lapansi, chifukwa sakuyenera kukhala ndi moyo!”+
22 Iwo anali kumumvetsera mpaka pa mawu amenewa. Kenako anafuula kuti: “Munthu ameneyu asapezekenso padziko lapansi, chifukwa sakuyenera kukhala ndi moyo!”+