Machitidwe 21:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Khamu la anthu linali kuwatsatira, likufuula kuti: “Aphedwe ameneyo!”+ Machitidwe 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero anapita kwa ansembe aakulu+ ndi kwa akulu kukanena kuti: “Ife tachita lumbiro ndi kudzitemberera kuti sitilawa chakudya kufikira titapha Paulo. Machitidwe 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Fesito ananena kuti: “Mfumu Agiripa ndi anthu nonse amene muli nafe pano, mukumuona munthu uyu. Ayuda onse anandipempha ine ku Yerusalemu komanso kuno, mofuula kuti iyeyu sayeneranso kukhala ndi moyo.+
14 Chotero anapita kwa ansembe aakulu+ ndi kwa akulu kukanena kuti: “Ife tachita lumbiro ndi kudzitemberera kuti sitilawa chakudya kufikira titapha Paulo.
24 Ndiyeno Fesito ananena kuti: “Mfumu Agiripa ndi anthu nonse amene muli nafe pano, mukumuona munthu uyu. Ayuda onse anandipempha ine ku Yerusalemu komanso kuno, mofuula kuti iyeyu sayeneranso kukhala ndi moyo.+