Machitidwe 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ali pa ulendo wakewo, anayandikira Damasiko. Mwadzidzidzi anangoona ngwee! kuwala kochokera kumwamba kutamuzungulira.+ Machitidwe 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Koma ndili m’njira, ndikuyandikira ku Damasiko, dzuwa lili pamutu, mwadzidzidzi kuwala kwakukulu kochokera kumwamba kunangoti ngwee! kuzungulira pamene ine ndinali.+
3 Ali pa ulendo wakewo, anayandikira Damasiko. Mwadzidzidzi anangoona ngwee! kuwala kochokera kumwamba kutamuzungulira.+
6 “Koma ndili m’njira, ndikuyandikira ku Damasiko, dzuwa lili pamutu, mwadzidzidzi kuwala kwakukulu kochokera kumwamba kunangoti ngwee! kuzungulira pamene ine ndinali.+