Machitidwe 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Makamaka chifukwa chakuti ndinu katswiri pa miyambo yonse,+ komanso pa zimene Ayuda amakangana. Choncho ndikukupemphani kuti mundimvetsere moleza mtima.
3 Makamaka chifukwa chakuti ndinu katswiri pa miyambo yonse,+ komanso pa zimene Ayuda amakangana. Choncho ndikukupemphani kuti mundimvetsere moleza mtima.