Yohane 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano anthu okhala naye pafupi ndi anthu ena amene m’mbuyomo anali kumuona akupemphapempha anayamba kunena kuti: “Si uyu kodi amene anali kukhala pansi n’kumapemphapempha uja?”+ Machitidwe 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno tsiku ndi tsiku anthu anali kunyamula mwamuna wina amene anabadwa ali wolumala.+ Iwo anali kukhazika wolumalayo pafupi ndi khomo la kachisi lotchedwa Chipata Chokongola,+ kuti azipempha mphatso zachifundo kwa olowa m’kachisimo.+
8 Tsopano anthu okhala naye pafupi ndi anthu ena amene m’mbuyomo anali kumuona akupemphapempha anayamba kunena kuti: “Si uyu kodi amene anali kukhala pansi n’kumapemphapempha uja?”+
2 Ndiyeno tsiku ndi tsiku anthu anali kunyamula mwamuna wina amene anabadwa ali wolumala.+ Iwo anali kukhazika wolumalayo pafupi ndi khomo la kachisi lotchedwa Chipata Chokongola,+ kuti azipempha mphatso zachifundo kwa olowa m’kachisimo.+