Machitidwe 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako anayamba kumuzindikira kuti ndi mwamuna amene anali kukhala pa Chipata Chokongola+ cha kachisi n’kumapempha mphatso zachifundo. Ndipo iwo anadabwa ndi kuzizwa kwambiri+ ndi zimene zinam’chitikirazo.
10 Kenako anayamba kumuzindikira kuti ndi mwamuna amene anali kukhala pa Chipata Chokongola+ cha kachisi n’kumapempha mphatso zachifundo. Ndipo iwo anadabwa ndi kuzizwa kwambiri+ ndi zimene zinam’chitikirazo.