Machitidwe 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho panabuka phokoso lalikulu,+ ndipo alembi ena a gulu la Afarisi anaimirira ndi kuyamba kutsutsa mwaukali kuti: “Sitikupeza cholakwa chilichonse mwa munthu ameneyu.+ Koma ngati mzimu kapena mngelo walankhula naye,+ . . .” Machitidwe 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kumeneko ndinapeza kuti akumuimba mlandu pa nkhani zokhudza Chilamulo chawo.+ Koma sanapezeke ndi mlandu uliwonse woyenera chilango cha imfa kapena kuponyedwa m’ndende.+ Machitidwe 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma ine ndinaona kuti sanachite chilichonse choyenera imfa.+ Choncho iyeyu atapempha kuti akaonekere kwa Wolemekezeka,+ ndinaganiza zomutumiza. Machitidwe 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma pochoka anayamba kukambirana kuti: “Munthu uyu sakuchita chilichonse choyenera imfa+ kapena kumangidwa.”
9 Choncho panabuka phokoso lalikulu,+ ndipo alembi ena a gulu la Afarisi anaimirira ndi kuyamba kutsutsa mwaukali kuti: “Sitikupeza cholakwa chilichonse mwa munthu ameneyu.+ Koma ngati mzimu kapena mngelo walankhula naye,+ . . .”
29 Kumeneko ndinapeza kuti akumuimba mlandu pa nkhani zokhudza Chilamulo chawo.+ Koma sanapezeke ndi mlandu uliwonse woyenera chilango cha imfa kapena kuponyedwa m’ndende.+
25 Koma ine ndinaona kuti sanachite chilichonse choyenera imfa.+ Choncho iyeyu atapempha kuti akaonekere kwa Wolemekezeka,+ ndinaganiza zomutumiza.
31 Koma pochoka anayamba kukambirana kuti: “Munthu uyu sakuchita chilichonse choyenera imfa+ kapena kumangidwa.”