Yesaya 56:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti Yehova wanena kuti: “Anthu ofulidwa amene amasunga sabata langa, ndiponso amene asankha kuchita zimene ndimasangalala nazo,+ komanso amene amatsatira pangano langa,+
4 Pakuti Yehova wanena kuti: “Anthu ofulidwa amene amasunga sabata langa, ndiponso amene asankha kuchita zimene ndimasangalala nazo,+ komanso amene amatsatira pangano langa,+