Yeremiya 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Kodi Mkusi*+ angasinthe khungu lake, kapena kodi kambuku angasinthe mawanga ake?+ Ngati angathe kuchita zimenezi, ndiye kuti inunso amene munaphunzitsidwa kuchita zinthu zoipa mungathe kuchita zinthu zabwino.+ Zefaniya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Anthu amene akundichonderera, anthu anga obalalitsidwa, adzandibweretsera mphatso kuchokera kuchigawo cha mitsinje ya ku Itiyopiya.+
23 “Kodi Mkusi*+ angasinthe khungu lake, kapena kodi kambuku angasinthe mawanga ake?+ Ngati angathe kuchita zimenezi, ndiye kuti inunso amene munaphunzitsidwa kuchita zinthu zoipa mungathe kuchita zinthu zabwino.+
10 “Anthu amene akundichonderera, anthu anga obalalitsidwa, adzandibweretsera mphatso kuchokera kuchigawo cha mitsinje ya ku Itiyopiya.+