Machitidwe 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndinazunza otsatira Njira imeneyi mpaka imfa.+ Ndinali kumanga amuna ndi akazi ndi kuwapereka kundende.+ Machitidwe 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthawi zambiri ndinawapatsa chilango m’masunagoge onse,+ poyesa kuwakakamiza kuti akane chikhulupiriro chawo. Popeza ndinali nditakwiya nawo kwambiri, ndinafika pa kuwazunza ngakhale m’mizinda yakunja.
4 Ndinazunza otsatira Njira imeneyi mpaka imfa.+ Ndinali kumanga amuna ndi akazi ndi kuwapereka kundende.+
11 Nthawi zambiri ndinawapatsa chilango m’masunagoge onse,+ poyesa kuwakakamiza kuti akane chikhulupiriro chawo. Popeza ndinali nditakwiya nawo kwambiri, ndinafika pa kuwazunza ngakhale m’mizinda yakunja.