Machitidwe 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ambuyewo anamuuza kuti: “Nyamuka, upite kumsewu wotchedwa Msewu Wowongoka. Ukakafika panyumba ya Yudasi, ukafunse za munthu wa ku Tariso, dzina lake Saulo.+ Iyeyo akupemphera,
11 Ambuyewo anamuuza kuti: “Nyamuka, upite kumsewu wotchedwa Msewu Wowongoka. Ukakafika panyumba ya Yudasi, ukafunse za munthu wa ku Tariso, dzina lake Saulo.+ Iyeyo akupemphera,