Machitidwe 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amuna amene anali nane+ anaonadi kuwalako, koma sanamve mawu a amene anali kulankhula ndi ine.+ Machitidwe 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ndili mumsewu dzuwa lili pamutu, Inu mfumu, ndinaona kuwala koposa kunyezimira kwa dzuwa kochokera kumwamba kutandizungulira pamodzi ndi amene ndinali nawo pa ulendowo.+
13 Koma ndili mumsewu dzuwa lili pamutu, Inu mfumu, ndinaona kuwala koposa kunyezimira kwa dzuwa kochokera kumwamba kutandizungulira pamodzi ndi amene ndinali nawo pa ulendowo.+