Yoswa 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pambuyo pake, mkaziyo anatulutsa amunawo powatsitsa ndi chingwe pawindo, pakuti mpanda wa mzindawo unalinso khoma* la nyumba yake, ndipo nyumba yakeyo inali pampandapo.+ 1 Samueli 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nthawi yomweyo, Mikala anathandiza Davide kutulukira pawindo kuti athawe ndi kupulumuka.+ 2 Akorinto 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 koma ndinaikidwa m’dengu n’kutsitsidwa pawindo la mpanda wa mzindawo,+ ndipo ndinapulumuka m’manja mwake.
15 Pambuyo pake, mkaziyo anatulutsa amunawo powatsitsa ndi chingwe pawindo, pakuti mpanda wa mzindawo unalinso khoma* la nyumba yake, ndipo nyumba yakeyo inali pampandapo.+
33 koma ndinaikidwa m’dengu n’kutsitsidwa pawindo la mpanda wa mzindawo,+ ndipo ndinapulumuka m’manja mwake.