1 Mbiri 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo anapitiriza kukhala ku Giliyadi,+ ku Basana,+ ndi m’midzi yake yozungulira+ komanso m’malo onse odyetsera ziweto a ku Sharoni, mpaka kumapeto kwa malo amenewa.
16 Iwo anapitiriza kukhala ku Giliyadi,+ ku Basana,+ ndi m’midzi yake yozungulira+ komanso m’malo onse odyetsera ziweto a ku Sharoni, mpaka kumapeto kwa malo amenewa.