Machitidwe 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma amuna ena oopa Mulungu anatenga Sitefano ndi kukamuika m’manda,+ ndipo anamulira kwambiri.+ Machitidwe 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Tsopano Hananiya, munthu woopa Mulungu malinga ndi Chilamulo, amene anali ndi mbiri yabwino+ pakati pa Ayuda onse okhala kumeneko,
12 “Tsopano Hananiya, munthu woopa Mulungu malinga ndi Chilamulo, amene anali ndi mbiri yabwino+ pakati pa Ayuda onse okhala kumeneko,