Machitidwe 9:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kwa masiku angapo Petulo anakhalabe mu Yopa+ kwa munthu wina wofufuta zikopa, dzina lake Simoni.+ Machitidwe 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chotero tumiza anthu ku Yopa, kuti akaitane Simoni wotchedwanso Petulo.+ Munthu ameneyo ndi mlendo m’nyumba ya Simoni wofufuta zikopa, amene amakhala m’mbali mwa nyanja.’+
32 Chotero tumiza anthu ku Yopa, kuti akaitane Simoni wotchedwanso Petulo.+ Munthu ameneyo ndi mlendo m’nyumba ya Simoni wofufuta zikopa, amene amakhala m’mbali mwa nyanja.’+