Ezekieli 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 M’chaka cha 30, m’mwezi wachinayi, pa tsiku lachisanu la mweziwo, pamene ndinali pakati pa anthu amene anali ku ukapolo+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara,+ kumwamba kunatseguka+ ndipo ndinayamba kuona masomphenya a Mulungu.+ Machitidwe 7:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Ndipo ananena kuti: “Taonani! Ndikuona kumwamba kotseguka,+ ndipo Mwana wa munthu+ waimirira kudzanja lamanja la Mulungu.”+ Chivumbulutso 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo nditayang’ana ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Wokwerapo wake dzina lake linali Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iyeyo anali kuweruza ndi kumenya nkhondo mwachilungamo.+
1 M’chaka cha 30, m’mwezi wachinayi, pa tsiku lachisanu la mweziwo, pamene ndinali pakati pa anthu amene anali ku ukapolo+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara,+ kumwamba kunatseguka+ ndipo ndinayamba kuona masomphenya a Mulungu.+
56 Ndipo ananena kuti: “Taonani! Ndikuona kumwamba kotseguka,+ ndipo Mwana wa munthu+ waimirira kudzanja lamanja la Mulungu.”+
11 Ndipo nditayang’ana ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Wokwerapo wake dzina lake linali Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iyeyo anali kuweruza ndi kumenya nkhondo mwachilungamo.+