Zekariya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Mitundu yambiri ya anthu idzadziphatika kwa Yehova pa tsikulo,+ choncho adzakhala anthu anga.+ Ine ndidzakhala mwa iwe.” Ndipo udzadziwa kuti Yehova wa makamu wandituma kwa iwe.+ Luka 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Maso anga aona kuwala+ kochotsa nsalu yophimba+ mitundu ya anthu+ ndi ulemerero wa anthu anu Aisiraeli.” Machitidwe 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atafika kumeneko ndi kusonkhanitsa pamodzi mpingo, anafotokoza+ zinthu zambiri zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwo. Anafotokozanso kuti Mulungu anatsegulira anthu a mitundu ina khomo lolowera m’chikhulupiriro chimenechi.+
11 “Mitundu yambiri ya anthu idzadziphatika kwa Yehova pa tsikulo,+ choncho adzakhala anthu anga.+ Ine ndidzakhala mwa iwe.” Ndipo udzadziwa kuti Yehova wa makamu wandituma kwa iwe.+
32 Maso anga aona kuwala+ kochotsa nsalu yophimba+ mitundu ya anthu+ ndi ulemerero wa anthu anu Aisiraeli.”
27 Atafika kumeneko ndi kusonkhanitsa pamodzi mpingo, anafotokoza+ zinthu zambiri zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwo. Anafotokozanso kuti Mulungu anatsegulira anthu a mitundu ina khomo lolowera m’chikhulupiriro chimenechi.+