Machitidwe 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Atafika ku Yerusalemu analandiridwa ndi manja awiri+ ndi mpingo, atumwi, komanso akulu. Kumeneko anafotokoza zinthu zambiri zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwo.+ Machitidwe 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Paulo anawalonjera ndi kuyamba kuwafotokozera mwatsatanetsatane+ zimene Mulungu anachita pakati pa anthu a mitundu ina kudzera mu utumiki wake.+
4 Atafika ku Yerusalemu analandiridwa ndi manja awiri+ ndi mpingo, atumwi, komanso akulu. Kumeneko anafotokoza zinthu zambiri zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwo.+
19 Paulo anawalonjera ndi kuyamba kuwafotokozera mwatsatanetsatane+ zimene Mulungu anachita pakati pa anthu a mitundu ina kudzera mu utumiki wake.+