Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Muzidya mkate wopanda chofufumitsa masiku 7. Tsiku loyamba muzichotsa m’nyumba zanu mtanda wa ufa wokanda wokhala ndi chofufumitsa chifukwa aliyense wakudya mkate wokhala ndi chofufumitsa, kuchokera pa tsiku loyamba kukafika pa tsiku la 7,+ munthu wotero adzaphedwa kuti asakhalenso mu Isiraeli.+

  • Ekisodo 23:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Muzichita chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda chofufumitsa+ masiku 7 pa nthawi yake m’mwezi wa Abibu,*+ monga momwe ndakulamulirani, chifukwa munatuluka mu Iguputo m’mwezi umenewu. Ndipo palibe ayenera kuonekera kwa ine chimanjamanja.+

  • Levitiko 23:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “‘Pa tsiku la 15 m’mwezi umenewu, muzichita chikondwerero cha Yehova cha mikate yopanda chofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda chofufumitsa imeneyi masiku 7.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena