Machitidwe 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno tsiku ndi tsiku anthu anali kunyamula mwamuna wina amene anabadwa ali wolumala.+ Iwo anali kukhazika wolumalayo pafupi ndi khomo la kachisi lotchedwa Chipata Chokongola,+ kuti azipempha mphatso zachifundo kwa olowa m’kachisimo.+
2 Ndiyeno tsiku ndi tsiku anthu anali kunyamula mwamuna wina amene anabadwa ali wolumala.+ Iwo anali kukhazika wolumalayo pafupi ndi khomo la kachisi lotchedwa Chipata Chokongola,+ kuti azipempha mphatso zachifundo kwa olowa m’kachisimo.+