Yesaya 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawiyo, munthu wolumala adzakwera phiri ngati mmene imachitira mbawala yamphongo.+ Lilime la munthu wosalankhula lidzafuula mokondwa.+ Pakuti m’chipululu mudzatumphuka madzi ndipo m’dera lachipululu mudzayenda mitsinje. Machitidwe 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo anadumpha n’kuimirira,+ ndi kuyamba kuyenda. Ndipo analowa nawo limodzi m’kachisimo,+ akuyenda, kudumphadumpha ndi kutamanda Mulungu.
6 Pa nthawiyo, munthu wolumala adzakwera phiri ngati mmene imachitira mbawala yamphongo.+ Lilime la munthu wosalankhula lidzafuula mokondwa.+ Pakuti m’chipululu mudzatumphuka madzi ndipo m’dera lachipululu mudzayenda mitsinje.
8 Pamenepo anadumpha n’kuimirira,+ ndi kuyamba kuyenda. Ndipo analowa nawo limodzi m’kachisimo,+ akuyenda, kudumphadumpha ndi kutamanda Mulungu.