Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano Herode atakonzeka kuti abweretse Petulo kwa anthu, usiku umenewo Petuloyo anali chigonere ali womangidwa ndi maunyolo awiri pakati pa asilikali awiri. Pakhomo panalinso alonda olondera ndende.

  • Machitidwe 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Atapitirira gulu loyamba la asilikali a pachipata ndi lachiwiri, anafika pachipata chachitsulo cholowera mumzinda, ndipo chinawatsegukira chokha.+ Pamene anatuluka anayendera limodzi msewu umodzi wokha, ndipo nthawi yomweyo mngelo uja anamuchokera.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena