Yohane 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 ndipo adzatuluka. Amene anali kuchita zabwino adzauka kuti alandire moyo.+ Amene anali kuchita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+ Yohane 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo Yesu anati: “Ine ndine kuuka ndi moyo.+ Aliyense wokhulupirira mwa ine, ngakhale amwalire, adzakhalanso ndi moyo.+ 1 Akorinto 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano ngati timalalikira kuti Khristu anaukitsidwa kwa akufa,+ bwanji ena mwa inu akunena kuti akufa sadzaukitsidwa?+ Chivumbulutso 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wodala+ ndi woyera+ ndiye aliyense wouka nawo pa kuuka koyamba. Pa iwo, imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi naye zaka 1,000.+
29 ndipo adzatuluka. Amene anali kuchita zabwino adzauka kuti alandire moyo.+ Amene anali kuchita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+
25 Pamenepo Yesu anati: “Ine ndine kuuka ndi moyo.+ Aliyense wokhulupirira mwa ine, ngakhale amwalire, adzakhalanso ndi moyo.+
12 Tsopano ngati timalalikira kuti Khristu anaukitsidwa kwa akufa,+ bwanji ena mwa inu akunena kuti akufa sadzaukitsidwa?+
6 Wodala+ ndi woyera+ ndiye aliyense wouka nawo pa kuuka koyamba. Pa iwo, imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi naye zaka 1,000.+