Yesaya 42:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 kuti ukatsegule maso a akhungu,+ ukatulutse mkaidi m’ndende ya mdima+ ndiponso kuti ukatulutse m’ndende anthu amene ali mu mdima.+ Mateyu 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Alekeni amenewo. Iwo ndi atsogoleri akhungu. Chotero ngati munthu wakhungu akutsogolera wakhungu mnzake, onse awiri adzagwera m’dzenje.”+ Mateyu 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Tsoka kwa inu atsogoleri akhungu,+ amene mumati, ‘Ngati munthu walumbirira kachisi palibe kanthu, koma ngati munthu walumbirira golide wa m’kachisi, asunge lumbiro lake.’+
7 kuti ukatsegule maso a akhungu,+ ukatulutse mkaidi m’ndende ya mdima+ ndiponso kuti ukatulutse m’ndende anthu amene ali mu mdima.+
14 Alekeni amenewo. Iwo ndi atsogoleri akhungu. Chotero ngati munthu wakhungu akutsogolera wakhungu mnzake, onse awiri adzagwera m’dzenje.”+
16 “Tsoka kwa inu atsogoleri akhungu,+ amene mumati, ‘Ngati munthu walumbirira kachisi palibe kanthu, koma ngati munthu walumbirira golide wa m’kachisi, asunge lumbiro lake.’+