2 Akorinto 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho sitikubwerera m’mbuyo. Koma ngakhale munthu wathu wakunja akutha, ndithudi munthu wathu wamkati+ akukhalitsidwanso watsopano tsiku ndi tsiku. Aefeso 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kutinso mogwirizana ndi chuma+ cha ulemerero wake, akuloleni kuti munthu wanu wamkati+ akhale wamphamvu, mwa mphamvu ya mzimu wake,+ Aefeso 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo munaphunzitsidwa kuti mukhale atsopano mu mphamvu yoyendetsa maganizo anu,+
16 Choncho sitikubwerera m’mbuyo. Koma ngakhale munthu wathu wakunja akutha, ndithudi munthu wathu wamkati+ akukhalitsidwanso watsopano tsiku ndi tsiku.
16 Kutinso mogwirizana ndi chuma+ cha ulemerero wake, akuloleni kuti munthu wanu wamkati+ akhale wamphamvu, mwa mphamvu ya mzimu wake,+